Genesis 49:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake achikhalire,+ ndipo manja ake anali amphamvu ndi ochenjera.+ M’busayo, Mwala wa Isiraeli,+ akuchokera m’manja mwa Wamphamvu wa Yakobo.+ M’busayo akuchokera kumeneko ndithu. Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+
24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake achikhalire,+ ndipo manja ake anali amphamvu ndi ochenjera.+ M’busayo, Mwala wa Isiraeli,+ akuchokera m’manja mwa Wamphamvu wa Yakobo.+ M’busayo akuchokera kumeneko ndithu.
3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+