Deuteronomo 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Anachita izi kuti achotse mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, ndi kulowetsamo inu, kukupatsani dziko lawo kuti likhale cholowa chanu monga mmene zilili lero.+ Deuteronomo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+
38 Anachita izi kuti achotse mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, ndi kulowetsamo inu, kukupatsani dziko lawo kuti likhale cholowa chanu monga mmene zilili lero.+
17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+