Hoseya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+ Habakuku 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 N’chifukwa chake mdaniyo amaperekera nsembe khoka lake ndipo amafukizira nsembe yautsi ukonde wake wophera nsomba. Iye amatero chifukwa chakuti amapeza chakudya chonona ndiponso chakudya chopatsa thanzi chifukwa cha khoka ndi ukonde wakewo.+ 1 Akorinto 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana+ ndi ena ndani? Inde, uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo,+ n’chifukwa chiyani ukudzitama+ ngati kuti sunachite kulandira?
8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+
16 N’chifukwa chake mdaniyo amaperekera nsembe khoka lake ndipo amafukizira nsembe yautsi ukonde wake wophera nsomba. Iye amatero chifukwa chakuti amapeza chakudya chonona ndiponso chakudya chopatsa thanzi chifukwa cha khoka ndi ukonde wakewo.+
7 Kodi akukupangitsa kukhala wosiyana+ ndi ena ndani? Inde, uli ndi chiyani chimene sunachite kulandira?+ Ndiye ngati unachita kulandira zinthu zimenezo,+ n’chifukwa chiyani ukudzitama+ ngati kuti sunachite kulandira?