Yohane 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Poyankha Yohane anati: “Munthu sangalandire kanthu kalikonse akapanda kupatsidwa kuchokera kumwamba.+ Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+
27 Poyankha Yohane anati: “Munthu sangalandire kanthu kalikonse akapanda kupatsidwa kuchokera kumwamba.+
17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+