Deuteronomo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+ Salimo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Usapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa.+Usakhumbe kukhala ngati anthu ochita zosalungama.+
17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+