1 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo. Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+
16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo.
24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+