1 Mafumu 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Panali akuluakulu oyang’anira nduna okwana 550 amene ankayang’anira ntchito ya Solomo. Iwowa anali akapitawo oyang’anira anthu ogwira ntchito.+
23 Panali akuluakulu oyang’anira nduna okwana 550 amene ankayang’anira ntchito ya Solomo. Iwowa anali akapitawo oyang’anira anthu ogwira ntchito.+