1 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo. 2 Mbiri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+ 2 Mbiri 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Panali akuluakulu oyang’anira nduna+ okwana 250 a Mfumu Solomo. Iwowa anali akapitawo oyang’anira anthu ogwira ntchito.+
16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo.
18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+
10 Panali akuluakulu oyang’anira nduna+ okwana 250 a Mfumu Solomo. Iwowa anali akapitawo oyang’anira anthu ogwira ntchito.+