1 Mafumu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumuyo inalamula kuti aseme miyala ikuluikulu yokwera mtengo,+ kuti akamange maziko+ a nyumbayo ndi miyala yosema.+ 1 Mafumu 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho amisiri omanga a Solomo ndi amisiri omanga a Hiramu ndiponso Agebala+ anasema miyalayo, ndipo anapitiriza kudula mitengo ndi kusema miyala pokonzekera kumanga nyumbayo. 1 Mbiri 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palinso antchito ambirimbiri, osema miyala,+ amisiri a miyala ndi a matabwa, ndiponso anthu onse odziwa ntchito zosiyanasiyana.+
17 Ndiyeno mfumuyo inalamula kuti aseme miyala ikuluikulu yokwera mtengo,+ kuti akamange maziko+ a nyumbayo ndi miyala yosema.+
18 Choncho amisiri omanga a Solomo ndi amisiri omanga a Hiramu ndiponso Agebala+ anasema miyalayo, ndipo anapitiriza kudula mitengo ndi kusema miyala pokonzekera kumanga nyumbayo.
15 Palinso antchito ambirimbiri, osema miyala,+ amisiri a miyala ndi a matabwa, ndiponso anthu onse odziwa ntchito zosiyanasiyana.+