1 Mafumu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.
7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.