Aefeso 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mogwirizana ndi iye, nyumba yonse, pokhala yolumikizana bwino,+ ikukula kukhala kachisi woyera wa Yehova.+ 1 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+
21 Mogwirizana ndi iye, nyumba yonse, pokhala yolumikizana bwino,+ ikukula kukhala kachisi woyera wa Yehova.+
5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+