Yesaya 56:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndidzawabweretsa kuphiri langa loyera+ ndi kuwasangalatsa m’nyumba yanga yopemphereramo.+ Nsembe zawo zopsereza zathunthu+ ndi nsembe zawo zina+ ndidzazilandira paguwa langa lansembe.+ Pakuti nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonse.”+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
7 ndidzawabweretsa kuphiri langa loyera+ ndi kuwasangalatsa m’nyumba yanga yopemphereramo.+ Nsembe zawo zopsereza zathunthu+ ndi nsembe zawo zina+ ndidzazilandira paguwa langa lansembe.+ Pakuti nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo anthu a mitundu yonse.”+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+