Akolose 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amatero koma osagwira mwamphamvu amene ali mutu,+ amene kuchokera kwa iye, thupi lonselo, limene limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ndi lolumikizika bwino+ mwa mfundo zake ndi minyewa, limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+
19 Amatero koma osagwira mwamphamvu amene ali mutu,+ amene kuchokera kwa iye, thupi lonselo, limene limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ndi lolumikizika bwino+ mwa mfundo zake ndi minyewa, limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+