Aefeso 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuchokera kwa iye, thupi lonselo+ limakula podzimanga lokha mwachikondi, pokhala lolumikizika bwino ndi logwirizana mwa mfundo iliyonse yogwira ntchito yake yofunikira, malinga ndi ntchito yoyenerera ya chiwalo chilichonse.+
16 Kuchokera kwa iye, thupi lonselo+ limakula podzimanga lokha mwachikondi, pokhala lolumikizika bwino ndi logwirizana mwa mfundo iliyonse yogwira ntchito yake yofunikira, malinga ndi ntchito yoyenerera ya chiwalo chilichonse.+