Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno udzamuuze kuti,

      “‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Munthu uyu+ dzina lake ndi Mphukira.+ Adzaphuka pamalo ake ndipo adzamanga kachisi wa Yehova.+

  • 1 Akorinto 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kodi inu simukudziwa kuti ndinu kachisi wa Mulungu,+ ndi kuti mzimu wa Mulungu ukukhala mwa inu?+

  • 1 Akorinto 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kodi zoona inu simukudziwa kuti thupi lanu ndilo kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu,+ umene munapatsidwa ndi Mulungu? Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena