Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+

  • Yesaya 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo.

  • Danieli 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Ndiyeno m’masomphenya ausikuwo, ndinaonanso wina wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera m’mitambo.+ Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri uja,+ ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Iye.+

  • Zekariya 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+

  • Maliko 15:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Tsopano, kapitawo wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyang’ana Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+

  • Yohane 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo Yesu anatulukira panja, atavala chisoti chachifumu chaminga chija ndi malaya akunja ofiirira. Ndipo Pilato anati: “Taonani! Mwamuna uja ndi uyu!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena