Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Limbani mtima anthu inu ndipo mukonzeke kugwira ntchito,+ inu amene mukumva mawu a aneneri masiku ano.+ Awa ndi mawu amene aneneriwo ananena pa tsiku limene maziko a nyumba ya Yehova wa makamu anayalidwa kuti kachisi amangidwe.+

  • Mateyu 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+

  • Aefeso 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mwamangidwa pamaziko+ a atumwi+ ndi aneneri,+ ndipo Khristu Yesuyo ndiye mwala wapakona wa mazikowo.+

  • Aheberi 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma Khristu monga Mwana+ wa mwiniwake wa nyumbayo, anali kuyang’anira nyumba ya Mulungu mokhulupirika. Ife ndife nyumba ya Mulunguyo,+ ngati tagwira mwamphamvu ufulu wathu wa kulankhula ndi kupitirizabe kunyadira chiyembekezocho mpaka mapeto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena