Aroma 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu. 1 Timoteyo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna otumikira bwino amakhala ndi mbiri yabwino+ ndi ufulu waukulu wa kulankhula+ za chikhulupiriro, mwa Khristu Yesu. Aheberi 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tikufuna kuti aliyense wa inu apitirize kuonetsa khama limene anali nalo poyamba, kuti chiyembekezo+ chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+
2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu.
13 Pakuti amuna otumikira bwino amakhala ndi mbiri yabwino+ ndi ufulu waukulu wa kulankhula+ za chikhulupiriro, mwa Khristu Yesu.
11 Koma tikufuna kuti aliyense wa inu apitirize kuonetsa khama limene anali nalo poyamba, kuti chiyembekezo+ chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+