Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ine ndine khomo.+ Aliyense wolowa kudzera mwa ine adzapulumuka, ndipo azidzalowa ndi kutuluka, kukapeza msipu.+

  • 2 Akorinto 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma zinthu zonse n’zochokera kwa Mulungu, amene anatigwirizanitsa+ ndi iyeyo kudzera mwa Khristu, ndipo anatipatsa utumiki+ wokhazikitsanso mtendere.

  • Aefeso 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+

  • Aefeso 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kudzera mwa iye, tili ndi ufulu wa kulankhula ndiponso njira yofikira Mulungu+ popanda kukayikira pokhala ndi chikhulupiriro mwa Yesuyo.

  • Aheberi 10:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena