Aroma 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu. 1 Akorinto 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi zoona inu simukudziwa kuti thupi lanu ndilo kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu,+ umene munapatsidwa ndi Mulungu? Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+
9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu.
19 Kodi zoona inu simukudziwa kuti thupi lanu ndilo kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu,+ umene munapatsidwa ndi Mulungu? Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+