Agalatiya 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngati tikukhala mwa mzimu, tiyeninso tipitirize kuyenda motsogoleredwa ndi mzimuwo.+