Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+

  • 1 Akorinto 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti palibe munthu wina amene angayale maziko ena+ alionse kupatulapo amene anayalidwawo, omwe ndi Yesu Khristu.+

  • 1 Petulo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+

  • Chivumbulutso 21:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mpanda wa mzindawo unalinso ndi miyala yomangira maziko+ yokwana 12, ndipo pamiyalayo panali mayina 12 a atumwi 12+ a Mwanawankhosa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena