1 Mafumu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumuyo inalamula kuti aseme miyala ikuluikulu yokwera mtengo,+ kuti akamange maziko+ a nyumbayo ndi miyala yosema.+ 1 Mafumu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga. 1 Mafumu 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyumba zonsezi, kuyambira pamaziko ake mpaka pamwamba pa khoma, ndiponso kuchokera panja pa nyumbazo mpaka kubwalo lalikulu,+ zinamangidwa ndi miyala yokwera mtengo+ yochita kuyeza, ndiponso yocheka ndi macheka a miyala, mkati ndi kunja komwe.
17 Ndiyeno mfumuyo inalamula kuti aseme miyala ikuluikulu yokwera mtengo,+ kuti akamange maziko+ a nyumbayo ndi miyala yosema.+
7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.
9 Nyumba zonsezi, kuyambira pamaziko ake mpaka pamwamba pa khoma, ndiponso kuchokera panja pa nyumbazo mpaka kubwalo lalikulu,+ zinamangidwa ndi miyala yokwera mtengo+ yochita kuyeza, ndiponso yocheka ndi macheka a miyala, mkati ndi kunja komwe.