1 Samueli 14:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+
52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+