Machitidwe 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli. Aheberi 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+
15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli.
4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+