-
Zekariya 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Kusala kudya kwa mʼmwezi wa 4,+ kusala kudya kwa mʼmwezi wa 5,+ kusala kudya kwa mʼmwezi wa 7+ ndiponso kusala kudya kwa mʼmwezi wa 10,+ idzakhala nthawi yachikondwerero komanso yosangalala kwa anthu a mʼnyumba ya Yuda.+ Choncho muzikonda choonadi ndiponso mtendere.’
-