25 Mʼmwezi wa 7, Isimaeli+ mwana wa Netaniya mwana wa Elisama, yemwe anali wa kubanja lachifumu* anapita kwa Gedaliya pamodzi ndi amuna 10. Iwo anapha Gedaliya ndi Ayuda ndiponso Akasidi amene anali naye ku Mizipa.+
5 “Kauze anthu onse amʼdzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munkasala kudya ndi kulira mʼmwezi wa 5 komanso mʼmwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munkasaladi kudya chifukwa cha ine?