Zekariya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Nsanja ya Olonda,11/15/1996, tsa. 5
5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+