Yeremiya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+ Zekariya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa makamu, kodi Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda imene munaikana ndi kuisiya kwa zaka 70,+ simuichitira chifundo kufikira liti?”+
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa makamu, kodi Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda imene munaikana ndi kuisiya kwa zaka 70,+ simuichitira chifundo kufikira liti?”+