Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+ Salimo 102:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+ Yesaya 64:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+
13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+
9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+