Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Zimenezi zinachitika pokwaniritsa mawu a Yehova amene ananena kudzera mwa Yeremiya,+ mpaka pamene dzikolo linalipira masabata ake.+ Masiku onse amene dzikolo linali bwinja linali kusunga sabata mpaka linakwaniritsa zaka 70.+

  • Danieli 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 m’chaka choyamba cha ulamuliro wake, ineyo Danieli ndinazindikira chiwerengero cha zaka za kuwonongedwa kwa Yerusalemu+ kuti zidzakhala zaka 70.+ Ndinazindikira zimenezi mwa kuwerenga mawu amene Yehova anauza mneneri Yeremiya+ olembedwa m’mabuku.

  • Zekariya 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Choncho mngelo wa Yehova anati: “Inu Yehova wa makamu, kodi Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda imene munaikana ndi kuisiya kwa zaka 70,+ simuichitira chifundo kufikira liti?”+

  • Zekariya 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena