Zekariya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kauze anthu onse amʼdzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munkasala kudya ndi kulira mʼmwezi wa 5 komanso mʼmwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munkasaladi kudya chifukwa cha ine? Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Nsanja ya Olonda,11/15/1996, tsa. 5
5 “Kauze anthu onse amʼdzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munkasala kudya ndi kulira mʼmwezi wa 5 komanso mʼmwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munkasaladi kudya chifukwa cha ine?