Yeremiya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno m’mwezi wachisanu, pa tsiku la 10 la mweziwo, m’chaka cha 19 cha ulamuliro wa Mfumu Nebukadirezara+ ya Babulo, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali kutumikira mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu. Zekariya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+
12 Ndiyeno m’mwezi wachisanu, pa tsiku la 10 la mweziwo, m’chaka cha 19 cha ulamuliro wa Mfumu Nebukadirezara+ ya Babulo, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali kutumikira mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu.
5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+