-
Salimo 30:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+
Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+
-
Yeremiya 31:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pamenepo iwo adzabwera ndi kufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+ Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa Yehova.+ Zidzawalanso chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano,+ mafuta, ana a nkhosa ndi ana a ng’ombe.+ Moyo wawo udzakhala ngati munda wothiriridwa bwino+ ndipo sadzakhalanso ofooka.”+
-
-
-