1 Samueli 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+
6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+