Salimo 74:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti. Maliro 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+
9 Zizindikiro zathu sitinazione, ndipo palibenso mneneri amene watsala,+Pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zikhala choncho mpaka liti.
9 Zipata+ zake zamira munthaka. Wawononga mipiringidzo yake ndipo waithyolathyola.Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa mitundu ina.+ Malamulo sakutsatiridwa.+Aneneri ake sakuonanso masomphenya ochokera kwa Yehova.+