1 Samueli 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chotero Sauli anayamba kufunsira kwa Mulungu, kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka m’manja mwa Isiraeli?”+ Koma Mulungu sanamuyankhe pa tsikuli.+ 1 Mbiri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sauli sanafunse kwa Yehova,+ chotero iye anamupha n’kupereka ufumuwo kwa Davide mwana wa Jese.+
37 Chotero Sauli anayamba kufunsira kwa Mulungu, kuti: “Kodi ndipite kwa Afilisiti?+ Kodi muwapereka m’manja mwa Isiraeli?”+ Koma Mulungu sanamuyankhe pa tsikuli.+