Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+ Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+ Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+ Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Mulungu alibe tsankho.+
14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+