Yobu 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi Mulungu angapotoze chiweruzo?+Ndipo kodi Wamphamvuyonse angapotoze chilungamo?+ Yakobo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu akakhala pa mayesero+ asamanene kuti: “Mulungu akundiyesa.” Pakuti Mulungu sangayesedwe ndi zinthu zoipa ndipo iye sayesa munthu ndi zinthu zoipa.
13 Munthu akakhala pa mayesero+ asamanene kuti: “Mulungu akundiyesa.” Pakuti Mulungu sangayesedwe ndi zinthu zoipa ndipo iye sayesa munthu ndi zinthu zoipa.