Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ukachoka pamenepo ufika kuphiri la Mulungu woona,+ kumene kuli mudzi wa asilikali+ a Afilisiti. Ndiyeno zimene zichitike n’zakuti, poyandikira mzindawo, ukumana ndi kagulu ka aneneri+ akuchokera kumalo okwezeka,+ akulankhula monga aneneri. Patsogolo pawo pakhala pali choimbira cha zingwe,+ maseche,+ chitoliro+ ndi zeze.+

  • 1 Mbiri 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Davide ndi atsogoleri+ a magulu a anthu otumikira,+ anapatula ena mwa ana a Asafu, a Hemani,+ ndi a Yedutuni,+ kuti azitumikira. Amuna atatuwa anali kulosera ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ ndi zinganga.+ Mwa ana awo anatengamo amuna ena n’kuwaika pa udindo kuti azitumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena