1 Mafumu 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo. Yesaya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+
40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo.
12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+