Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chifukwa asiya kumutsatira,+

      Ndipo sasamala za njira zake zonse,+

  • Salimo 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+

      Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+

  • Salimo 28:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pakuti iwo salabadira zochita za Yehova,+

      Kapena ntchito za manja ake.+

      Mulungu sadzawamanga koma adzawapasula.

  • Salimo 92:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Munthu wopanda nzeru sangadziwe zimenezi,+

      Ndipo munthu wopusa sangazimvetse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena