Salimo 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti iwo salabadira zochita za Yehova,+Kapena ntchito za manja ake.+Mulungu sadzawamanga koma adzawapasula. Yesaya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+
5 Pakuti iwo salabadira zochita za Yehova,+Kapena ntchito za manja ake.+Mulungu sadzawamanga koma adzawapasula.
12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+