Yesaya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+ Yesaya 30:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu inu mudzaimba nyimbo,+ ngati imene imaimbidwa usiku umene munthu amadziyeretsa pokonzekera chikondwerero.+ Mudzakhalanso ndi chimwemwe mumtima ngati munthu amene akuimba chitoliro+ popita kuphiri la Yehova,+ Thanthwe la Isiraeli.+
12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe, maseche, ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.+ Koma sayang’ana ntchito ya Yehova, ndipo ntchito ya manja ake saiona.+
29 Anthu inu mudzaimba nyimbo,+ ngati imene imaimbidwa usiku umene munthu amadziyeretsa pokonzekera chikondwerero.+ Mudzakhalanso ndi chimwemwe mumtima ngati munthu amene akuimba chitoliro+ popita kuphiri la Yehova,+ Thanthwe la Isiraeli.+