1 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+ Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+
4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+