Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kodi pali Mulungu winanso woposa Yehova?+Kodi pali thanthwe linanso loposa Mulungu wathu?+ Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+ Yesaya 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu muzidalira Yehova+ nthawi zonse, pakuti Ya* Yehova ndiye Thanthwe+ mpaka kalekale.
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+