1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+ 2 Samueli 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi pali Mulungu winanso woposa Yehova?+Kodi pali thanthwe linanso loposa Mulungu wathu?+ Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+ Yesaya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,
2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,