Deuteronomo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti thanthwe lawo silofanana ndi Thanthwe lathu,+Ndipo adani athu angavomereze zimenezi.+ 1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+ Salimo 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kodi pali Mulungu winanso woposa Yehova?+Kodi pali thanthwe linanso loposa Mulungu wathu?+ Salimo 94:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yehova adzakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndipo Mulungu wanga adzakhala thanthwe langa lothawirako.+ Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+
2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
22 Koma Yehova adzakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndipo Mulungu wanga adzakhala thanthwe langa lothawirako.+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+