Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nthawi yomweyo, Sauli anatumiza amithenga kuti akagwire Davide. Amithengawo ataona aneneri achikulire akunenera, Samueli ataima pakati pawo kuwatsogolera, mzimu+ wa Mulungu unafika pa amithenga a Sauli aja, ndipo nawonso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri.+

  • 2 Mafumu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno ana a aneneri+ amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo.+ Khalani chete.”

  • 2 Mafumu 4:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Pambuyo pake, Elisa anabwerera ku Giligala,+ ndipo m’dzikolo munali njala.+ Tsopano ana+ a aneneri anakhala pamaso pake.+ Patapita nthawi, iye anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”+

  • 2 Mafumu 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano ana+ a aneneri anauza Elisa kuti: “Taonani, malo+ amene tikukhala pamaso panu pano tikupanikizanapo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena