2 Mafumu 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pambuyo pake, Elisa anabwerera ku Giligala,+ ndipo m’dzikolo munali njala.+ Tsopano ana+ a aneneri anakhala pamaso pake.+ Patapita nthawi, iye anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”+
38 Pambuyo pake, Elisa anabwerera ku Giligala,+ ndipo m’dzikolo munali njala.+ Tsopano ana+ a aneneri anakhala pamaso pake.+ Patapita nthawi, iye anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”+